Yobu 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye watchinga njira yanga ndi mpanda wamiyala+ mwakuti sindingathe kudutsa.Ndiponso waika mdima panjira zanga.+ Salimo 88:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anzanga mwawaika kutali ndi ine.+Mwandisandutsa chinthu chonyansa kwa iwo.+Ndatsekerezedwa ndipo sindingathenso kuchoka.+ Hoseya 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Tsopano ine ndikutsekereza njira yake ndi mpanda waminga, ndipo ndidzamumangira mpanda wamiyala+ ndi kumutsekereza kuti asapeze njira zake.+
8 Iye watchinga njira yanga ndi mpanda wamiyala+ mwakuti sindingathe kudutsa.Ndiponso waika mdima panjira zanga.+
8 Anzanga mwawaika kutali ndi ine.+Mwandisandutsa chinthu chonyansa kwa iwo.+Ndatsekerezedwa ndipo sindingathenso kuchoka.+
6 “Tsopano ine ndikutsekereza njira yake ndi mpanda waminga, ndipo ndidzamumangira mpanda wamiyala+ ndi kumutsekereza kuti asapeze njira zake.+