Yobu 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iyetu amagwetsa zinthu kuti zisamangidwe,+Zimene iye watseka, palibe munthu amene angazitsegule.+ Yobu 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye watchinga njira yanga ndi mpanda wamiyala+ mwakuti sindingathe kudutsa.Ndiponso waika mdima panjira zanga.+ Maliro 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Watsekereza njira zanga ndi miyala yosema.+ Wachititsa njira zanga kukhala zovuta kuyendamo.+ Hoseya 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Tsopano ine ndikutsekereza njira yake ndi mpanda waminga, ndipo ndidzamumangira mpanda wamiyala+ ndi kumutsekereza kuti asapeze njira zake.+
8 Iye watchinga njira yanga ndi mpanda wamiyala+ mwakuti sindingathe kudutsa.Ndiponso waika mdima panjira zanga.+
6 “Tsopano ine ndikutsekereza njira yake ndi mpanda waminga, ndipo ndidzamumangira mpanda wamiyala+ ndi kumutsekereza kuti asapeze njira zake.+