13 Ng’ambani mitima yanu+ osati zovala zanu+ ndipo bwererani kwa Yehova Mulungu wanu pakuti iye ndi wachisomo, wachifundo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha.+ Ndithu, iye adzakumverani chisoni chifukwa cha tsokalo.+
3 “Uwauze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “‘Bwererani kwa ine,’+ watero Yehova wa makamu, ‘ndipo ine ndidzabwerera kwa inu,’+ akutero Yehova wa makamu.”’