Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Anapitiriza kumuyendetsa pamapiri a dziko lapansi,+

      Moti anadya zokolola za m’minda.+

      Anapitirizanso kumudyetsa uchi wochokera m’thanthwe,+

      Ndi mafuta ochokera m’mwala wa nsangalabwi.+

  • Nehemiya 9:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Iwo analanda mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+ Analandanso nthaka yachonde,+ nyumba zodzaza ndi zinthu zonse zabwino,+ zitsime,*+ minda ya mpesa ndi ya maolivi+ ndi mitengo ya zipatso yochuluka. Atatero, anayamba kudya, kukhuta,+ kunenepa+ ndi kukondwera ndi ubwino wanu waukulu.+

  • Luka 15:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Nzeru zitam’bwerera, anati, ‘Komatu aganyu ambiri a bambo ali ndi chakudya chochuluka, koma ine kuno ndikufa ndi njala!

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena