Salimo 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, mwanditulutsa m’Manda,+Mwandisunga ndi moyo, kuti ndisatsikire m’dzenje.+ Salimo 49:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma Mulungu adzawombola moyo wanga ku Manda,+Pakuti adzandilandira. [Seʹlah.] Salimo 69:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yandikirani moyo wanga ndi kuupulumutsa.+Ndiwomboleni kwa adani anga.+