Nahumu 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mzindawu auchititsa kukhala wopanda kanthu ndipo ausandutsa bwinja.+ Mitima yawo yasungunuka ndi mantha.+ Mawondo awo akunjenjemera+ ndipo akumva ululu thupi lonse.+ Nkhope zawo zonse zili ndi nkhawa.+
10 Mzindawu auchititsa kukhala wopanda kanthu ndipo ausandutsa bwinja.+ Mitima yawo yasungunuka ndi mantha.+ Mawondo awo akunjenjemera+ ndipo akumva ululu thupi lonse.+ Nkhope zawo zonse zili ndi nkhawa.+