Nahumu 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mzindawu watsala wopanda kanthu, wawonongedwa ndipo wakhala bwinja.+ Mitima yawo yasungunuka ndi mantha, mawondo ndi ziuno zawo zikunjenjemera.Nkhope zawo zonse zili ndi nkhawa. Nahumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:10 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, tsa. 28
10 Mzindawu watsala wopanda kanthu, wawonongedwa ndipo wakhala bwinja.+ Mitima yawo yasungunuka ndi mantha, mawondo ndi ziuno zawo zikunjenjemera.Nkhope zawo zonse zili ndi nkhawa.