Nahumu 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mzindawu auchititsa kukhala wopanda kanthu ndipo ausandutsa bwinja.+ Mitima yawo yasungunuka ndi mantha.+ Mawondo awo akunjenjemera+ ndipo akumva ululu thupi lonse.+ Nkhope zawo zonse zili ndi nkhawa.+ Nahumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:10 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, tsa. 28
10 Mzindawu auchititsa kukhala wopanda kanthu ndipo ausandutsa bwinja.+ Mitima yawo yasungunuka ndi mantha.+ Mawondo awo akunjenjemera+ ndipo akumva ululu thupi lonse.+ Nkhope zawo zonse zili ndi nkhawa.+