Deuteronomo 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Muamoni kapena Mmowabu asalowe mumpingo wa Yehova.+ Ana awo asalowe mumpingo wa Yehova kufikira m’badwo wa 10, ngakhalenso mpaka kalekale. 2 Mbiri 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pambuyo pake ana a Mowabu,+ ana a Amoni,+ pamodzi ndi Aamonimu+ ena, anabwera kudzamenyana ndi Yehosafati.+
3 “Muamoni kapena Mmowabu asalowe mumpingo wa Yehova.+ Ana awo asalowe mumpingo wa Yehova kufikira m’badwo wa 10, ngakhalenso mpaka kalekale.
20 Pambuyo pake ana a Mowabu,+ ana a Amoni,+ pamodzi ndi Aamonimu+ ena, anabwera kudzamenyana ndi Yehosafati.+