2 Mafumu 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pomalizira pake Yehoasi anagona pamodzi ndi makolo ake, ndipo Yerobowamu*+ anakhala pampando wake wachifumu. Kenako Yehoasi anaikidwa m’manda ku Samariya pamodzi ndi mafumu a Isiraeli.+
13 Pomalizira pake Yehoasi anagona pamodzi ndi makolo ake, ndipo Yerobowamu*+ anakhala pampando wake wachifumu. Kenako Yehoasi anaikidwa m’manda ku Samariya pamodzi ndi mafumu a Isiraeli.+