2 Mafumu 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pomalizira pake Yehu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anamuika m’manda ku Samariya. Kenako Yehoahazi+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake. 2 Mafumu 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pomalizira pake Yehoahazi anagona pamodzi ndi makolo ake, ndipo anamuika m’manda ku Samariya.+ Kenako Yehoasi+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
35 Pomalizira pake Yehu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anamuika m’manda ku Samariya. Kenako Yehoahazi+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
9 Pomalizira pake Yehoahazi anagona pamodzi ndi makolo ake, ndipo anamuika m’manda ku Samariya.+ Kenako Yehoasi+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.