Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mawa m’mawa, mubwere fuko ndi fuko. Fuko limene Yehova adzasankhe+ lidzabwere patsogolo. Kenako mbumba ndi mbumba, ndipo mbumba imene Yehova adzasankhe idzabwere patsogolo. Kenako banja ndi banja, ndipo banja limene Yehova adzasankhe lidzabwere patsogolo, komanso mwamuna aliyense wamphamvu payekhapayekha.

  • 1 Samueli 14:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Kenako Sauli anati: “Chitani maere+ pakati pa ine ndi Yonatani mwana wanga.” Zitatero, maerewo anagwera Yonatani.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena