Miyambo 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Maere amaponyedwa pamwendo,+ koma zonse zimene maerewo amasonyeza zimachokera kwa Yehova.+ Yona 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno anayamba kuuzana kuti: “Tiyeni tichite maere+ kuti tidziwe amene wachititsa kuti tsoka limeneli litigwere.”+ Iwo anachitadi maere ndipo maerewo anagwera Yona.+
7 Ndiyeno anayamba kuuzana kuti: “Tiyeni tichite maere+ kuti tidziwe amene wachititsa kuti tsoka limeneli litigwere.”+ Iwo anachitadi maere ndipo maerewo anagwera Yona.+