Miyambo 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Maere amaponyedwa pamwendo,+ koma zonse zimene maerewo amasonyeza zimachokera kwa Yehova.+ Miyambo 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Maere amathetsa mikangano,+ ndipo amalekanitsa ngakhale anthu amphamvu.+ Machitidwe 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo atawononga mitundu 7 m’dziko la Kanani, anagawa dzikolo kwa Aisiraeli mwa kuchita maere.+