Luka 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa lero wakubadwirani Mpulumutsi,+ amene ndi Khristu Ambuye,+ mumzinda wa Davide.+ Yohane 7:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Kodi Malemba sanena kuti Khristu adzatuluka mwa ana a Davide,+ komanso mu Betelehemu+ mudzi umene Davide anali kukhala?”+
42 Kodi Malemba sanena kuti Khristu adzatuluka mwa ana a Davide,+ komanso mu Betelehemu+ mudzi umene Davide anali kukhala?”+