Yesaya 41:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Taona! Ndakusandutsa chopunthira mbewu,+ chida chatsopano chopunthira mbewu chokhala ndi mano. Udzapondaponda mapiri n’kuwaphwanya, ndipo zitunda udzazisandutsa mankhusu.+ Zekariya 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Onsewa adzakhala ngati amuna amphamvu+ opondaponda matope a m’misewu ya kunkhondo.+ Iwo adzamenya nkhondo pakuti Yehova ali nawo.+ Adani awo oyenda pamahatchi adzachita manyazi.+
15 “Taona! Ndakusandutsa chopunthira mbewu,+ chida chatsopano chopunthira mbewu chokhala ndi mano. Udzapondaponda mapiri n’kuwaphwanya, ndipo zitunda udzazisandutsa mankhusu.+
5 Onsewa adzakhala ngati amuna amphamvu+ opondaponda matope a m’misewu ya kunkhondo.+ Iwo adzamenya nkhondo pakuti Yehova ali nawo.+ Adani awo oyenda pamahatchi adzachita manyazi.+