Deuteronomo 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “M’thumba lako, usakhale ndi miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu,+ usakhale ndi muyezo waukulu ndi wina waung’ono. Miyambo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Sikelo yachinyengo imam’nyansa Yehova,+ koma mwala woyezera, wolemera mokwanira, umam’sangalatsa. Miyambo 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu ndiponso miyezo iwiri yosiyana ya efa,*+ zonsezi n’zonyansa kwa Yehova.+ Hoseya 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’manja mwa wamalonda muli sikelo yachinyengo+ ndipo iye amakonda kuba mwachinyengo.+
13 “M’thumba lako, usakhale ndi miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu,+ usakhale ndi muyezo waukulu ndi wina waung’ono.
10 Miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu ndiponso miyezo iwiri yosiyana ya efa,*+ zonsezi n’zonyansa kwa Yehova.+