Ezekieli 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana ku Yerusalemu ndipo ulankhule+ kwa malo oyera.+ Ulosere zoipa zimene zidzachitikire dziko la Isiraeli.+ Machitidwe 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komabe, kuti nkhaniyi isapitirire kufalikira kwa anthu ena, tiyeni tiwaopseze kuti asalankhulenso m’dzina limeneli kwa munthu wina aliyense.”+
2 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana ku Yerusalemu ndipo ulankhule+ kwa malo oyera.+ Ulosere zoipa zimene zidzachitikire dziko la Isiraeli.+
17 Komabe, kuti nkhaniyi isapitirire kufalikira kwa anthu ena, tiyeni tiwaopseze kuti asalankhulenso m’dzina limeneli kwa munthu wina aliyense.”+