Deuteronomo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Sankhani amuna anzeru, aluso+ ndi ozindikira+ m’mafuko anu, kuti ndiwaike kukhala atsogoleri anu.’+ 1 Akorinto 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikulankhula choncho kuti ndikuchititseni manyazi.+ Kodi zoona palibe wanzeru ndi mmodzi yemwe+ pakati panu amene angaweruze mlandu pakati pa abale ake?
13 Sankhani amuna anzeru, aluso+ ndi ozindikira+ m’mafuko anu, kuti ndiwaike kukhala atsogoleri anu.’+
5 Ndikulankhula choncho kuti ndikuchititseni manyazi.+ Kodi zoona palibe wanzeru ndi mmodzi yemwe+ pakati panu amene angaweruze mlandu pakati pa abale ake?