Salimo 55:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa cha zimene adani akunena, ndiponso chifukwa chakuti oipa andipanikiza.+Pakuti akundikhuthulira mavuto,+Ndipo mwaukali akundisungira chidani.+ Salimo 120:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimalimbikitsa mtendere,+ koma ndikalankhula,Iwo amafuna nkhondo.+ Salimo 140:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu amene amakonza chiwembu mumtima mwawo,+Amene amandiukira tsiku lonse ngati mmene zimakhalira pankhondo.+
3 Chifukwa cha zimene adani akunena, ndiponso chifukwa chakuti oipa andipanikiza.+Pakuti akundikhuthulira mavuto,+Ndipo mwaukali akundisungira chidani.+
2 Anthu amene amakonza chiwembu mumtima mwawo,+Amene amandiukira tsiku lonse ngati mmene zimakhalira pankhondo.+