Nahumu 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wa makamu akuti, “Taona! Ine ndikukuukira,+ ndipo nditentha magaleta ako ankhondo moti padzakhala utsi wambiri.+ Lupanga lidzadya mikango yako yamphamvu.+ Sudzasakanso nyama padziko lapansi,* ndipo mawu a amithenga ako sadzamvekanso.”+
13 Yehova wa makamu akuti, “Taona! Ine ndikukuukira,+ ndipo nditentha magaleta ako ankhondo moti padzakhala utsi wambiri.+ Lupanga lidzadya mikango yako yamphamvu.+ Sudzasakanso nyama padziko lapansi,* ndipo mawu a amithenga ako sadzamvekanso.”+