Deuteronomo 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndikanoladi lupanga langa lonyezimira,+Dzanja langa likagwira chiweruzo,+Ndidzalipsira adani anga,+Ndipo ndidzabwezera chilango kwa odana nane kwambiri.+ Ezekieli 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Lupanga lanoledwa pokonzekera kupha anthu. Lapukutidwa kuti linyezimire.’”’”+ “Koma kodi tilibe chifukwa chosangalalira?”+ “‘Kodi lupangalo likukana ndodo yachifumu+ ya mwana wanga,+ ngati mmene likukanira mtengo uliwonse?+
41 Ndikanoladi lupanga langa lonyezimira,+Dzanja langa likagwira chiweruzo,+Ndidzalipsira adani anga,+Ndipo ndidzabwezera chilango kwa odana nane kwambiri.+
10 Lupanga lanoledwa pokonzekera kupha anthu. Lapukutidwa kuti linyezimire.’”’”+ “Koma kodi tilibe chifukwa chosangalalira?”+ “‘Kodi lupangalo likukana ndodo yachifumu+ ya mwana wanga,+ ngati mmene likukanira mtengo uliwonse?+