Salimo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti inu sindinu Mulungu wokondwera ndi zoipa,+Palibe munthu woipa amene angakhale ndi inu ngakhale kwa kanthawi kochepa.+ Yesaya 59:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ayi si choncho. Koma zolakwa za anthu inu n’zimene zakulekanitsani ndi Mulungu wanu,+ ndipo machimo anu amuchititsa kuti akubisireni nkhope yake, kuti asamve zimene mukunena.+ 1 Petulo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma khalani motsanzira Woyera amene anakuitanani. Inunso khalani oyera m’makhalidwe anu onse,+
4 Pakuti inu sindinu Mulungu wokondwera ndi zoipa,+Palibe munthu woipa amene angakhale ndi inu ngakhale kwa kanthawi kochepa.+
2 Ayi si choncho. Koma zolakwa za anthu inu n’zimene zakulekanitsani ndi Mulungu wanu,+ ndipo machimo anu amuchititsa kuti akubisireni nkhope yake, kuti asamve zimene mukunena.+