Yesaya 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anafuula mwamphamvu ngati kubangula kwa mkango,+ kuti: “Inu Yehova, ine ndimaimirira tsiku lonse pansanja ya mlonda, ndipo usiku uliwonse ndimakhala pamalo anga olonderapo.+ Yesaya 62:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwe Yerusalemu, ine ndaika alonda pamakoma a mpanda wako.+ Nthawi zonse, tsiku lonse lathunthu ndi usiku wonse wathunthu, iwo asakhale chete.+ “Inu amene mukutchula dzina la Yehova,+ musakhale chete.+
8 Kenako anafuula mwamphamvu ngati kubangula kwa mkango,+ kuti: “Inu Yehova, ine ndimaimirira tsiku lonse pansanja ya mlonda, ndipo usiku uliwonse ndimakhala pamalo anga olonderapo.+
6 Iwe Yerusalemu, ine ndaika alonda pamakoma a mpanda wako.+ Nthawi zonse, tsiku lonse lathunthu ndi usiku wonse wathunthu, iwo asakhale chete.+ “Inu amene mukutchula dzina la Yehova,+ musakhale chete.+