Ekisodo 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pofika pano ndikanatambasula kale dzanja langa ndi kukupha ndi mliri, iweyo ndi anthu ako, kukufafanizani padziko lapansi.+ Numeri 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiwagwetsera mliri ndi kuwafafaniza, ndipo iwe ndidzakusandutsa mtundu waukulu ndi wamphamvu kuposa iwowa.”+ Numeri 16:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Kenako Mose anauza Aroni kuti: “Tenga chofukizira uikemo moto wochokera paguwa lansembe.+ Uikemo nsembe yofukiza n’kupita kwa khamulo mofulumira kuti ukawaphimbire machimo awo.+ Chita zimenezi chifukwa Yehova wakwiya kwambiri.+ Mliritu wayamba kale!” Numeri 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amene anaphedwa ndi mliriwo analipo 24,000.+
15 Pofika pano ndikanatambasula kale dzanja langa ndi kukupha ndi mliri, iweyo ndi anthu ako, kukufafanizani padziko lapansi.+
12 Ndiwagwetsera mliri ndi kuwafafaniza, ndipo iwe ndidzakusandutsa mtundu waukulu ndi wamphamvu kuposa iwowa.”+
46 Kenako Mose anauza Aroni kuti: “Tenga chofukizira uikemo moto wochokera paguwa lansembe.+ Uikemo nsembe yofukiza n’kupita kwa khamulo mofulumira kuti ukawaphimbire machimo awo.+ Chita zimenezi chifukwa Yehova wakwiya kwambiri.+ Mliritu wayamba kale!”