Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Atatero Mose anauza Aroni ndi ana ake ena, Eleazara ndi Itamara, kuti: “Musalekerere tsitsi lanu osalisamala,+ ndipo musang’ambe zovala zanu kuti mungafe ndiponso kuti Mulungu angakwiyire khamu lonseli.+ Abale anu, nyumba yonse ya Isiraeli ndiwo alire chifukwa cha kuwononga ndi moto kumene Yehova wachita.

  • Numeri 1:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 Alevi azimanga mahema awo mozungulira chihema cha Umboni kuti mkwiyo+ wa Mulungu usawayakire ana a Isiraeli. Aleviwo azitumikira pachihema cha Umbonicho.”+

  • Numeri 18:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Muzichita utumiki wanu m’malo oyera+ ndi paguwa lansembe,+ kuti mkwiyo+ usadzawabukirenso ana a Isiraeli.

  • 1 Mbiri 27:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Yowabu+ mwana wa Zeruya anayamba kuwerenga anthu koma sanamalize.+ Kenako mkwiyo+ wa Mulungu unagwera Isiraeli chifukwa chowerenga anthuwo, ndipo chiwerengerocho sichinalembedwe pa zochitika za m’masiku a Mfumu Davide.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena