Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 27:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 M’chihema chokumanako,* kunja kwa nsalu yotchinga+ pafupi ndi Umboni, Aroni ndi ana ake azikhazika nyale pamalo ake, kuunikira pamaso pa Yehova,+ kuyambira madzulo mpaka m’mawa. Limeneli ndi lamulo kwa ana a Isiraeli+ kuti mibadwo yawo izichita zimenezi mpaka kalekale.+

  • Ekisodo 30:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Aroni azifukiza zofukiza zonunkhira paguwapo.+ M’mawa uliwonse akamasamalira nyale,+ azifukiza zofukizazo.

  • Levitiko 24:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Aroni azikhazika nyale pamalo ake, kunja kwa nsalu yotchinga ya Umboni m’chihema chokumanako. Nyaleyo iziunikira pamaso pa Yehova nthawi zonse kuyambira madzulo mpaka m’mawa. Limeneli ndi lamulo kwa inu mpaka kalekale m’mibadwo yanu yonse.

  • Numeri 3:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Mkulu wa atsogoleri onse a Alevi anali Eleazara,+ mwana wa wansembe Aroni. Iye ndiye anali kuyang’anira onse otumikira pamalo oyera.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena