21 Mʼchihema chokumanako, kunja kwa katani imene ili pafupi ndi Umboni,+ Aroni ndi ana ake azionetsetsa kuti nyale zikuyaka pamaso pa Yehova, kuyambira madzulo mpaka mʼmawa.+ Limeneli ndi lamulo kwa Aisiraeli kuti mibadwo yawo izichita zimenezi mpaka kalekale.”+