Numeri 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Aleviwo azichita utumiki wawo pachihema chokumanako, ndipo ndi amene aziyankha mlandu wa zolakwa za anthuwo.+ Iwo asakhale ndi cholowa pakati pa Aisiraeli.+ Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale mʼmibadwo yanu yonse.
23 Aleviwo azichita utumiki wawo pachihema chokumanako, ndipo ndi amene aziyankha mlandu wa zolakwa za anthuwo.+ Iwo asakhale ndi cholowa pakati pa Aisiraeli.+ Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale mʼmibadwo yanu yonse.