Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndiyeno aziing’amba pakati cham’mapiko mwake, koma osailekanitsa.+ Kenako wansembe aziitentha paguwa lansembe pamwamba pa nkhuni zimene zili pamoto. Imeneyi ndi nsembe yopsereza,+ nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.+

  • Levitiko 21:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Lankhula ndi Aroni kuti, ‘Munthu aliyense mwa ana ako, ku mibadwo yawo yonse, amene ali ndi chilema+ asayandikire malo opatulika kudzapereka mkate wa Mulungu wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena