Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 8:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “Lamulo lokhudza Alevi ndi ili: Kuyambira wazaka 25 kupita m’tsogolo azilowa m’gulu la otumikira m’chihema chokumanako.

  • Numeri 18:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Azitumikira inuyo ndi kugwira ntchito zawo za pachihema chonse.+ Koma asamayandikire zipangizo za m’malo oyera, kapena kuyandikira guwa lansembe kuti iwowo kapena inuyo mungafe.+

  • Numeri 31:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Pa hafu imene ana a Isiraeli ati alandire, mutengepo chamoyo chimodzi pa zamoyo 50 zilizonse, pa anthu, ng’ombe, abulu, ndi nkhosa, ndi pa ziweto za mtundu uliwonse. Muzipereke kwa Alevi,+ amene amatumikira pachihema cha Yehova chopatulika.”+

  • 1 Mbiri 23:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ana a Leviwa analinso ndi ntchito yolondera+ chihema chokumanako, malo oyera,+ ndiponso yolondera abale awo, ana a Aroni, pa utumiki wa panyumba ya Yehova.+

  • 2 Mbiri 13:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma ife, Yehova ndiye Mulungu wathu+ ndipo sitinamusiye. Ansembe, omwe ndi ana a Aroni, akutumikira Yehova, ndiponso Alevi akugwira ntchito yawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena