Ekisodo 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu adzamva+ ndipo adzatekeseka.+Okhala ku Filisitiya adzamva zopweteka ngati za pobereka.+ Numeri 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Amowabu anakalankhula ndi akuluakulu a ku Midiyani,+ kuti: “Chikhamuchi chidzamwetula malo athu onse monga ng’ombe yomwetula msipu kubusa.” Pa nthawi imeneyo, Balaki+ mwana wa Zipori ndiye anali mfumu ya Mowabu.
4 Pamenepo Amowabu anakalankhula ndi akuluakulu a ku Midiyani,+ kuti: “Chikhamuchi chidzamwetula malo athu onse monga ng’ombe yomwetula msipu kubusa.” Pa nthawi imeneyo, Balaki+ mwana wa Zipori ndiye anali mfumu ya Mowabu.