Yesaya 60:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+ Mateyu 13:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mwana wa munthu adzatumiza angelo ake, ndipo adzachotsa mu ufumu wake zinthu zonse zopunthwitsa+ ndiponso anthu osamvera malamulo.
21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+
41 Mwana wa munthu adzatumiza angelo ake, ndipo adzachotsa mu ufumu wake zinthu zonse zopunthwitsa+ ndiponso anthu osamvera malamulo.