Salimo 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma kuchokera kumwamba, Yehova wayang’ana ana a anthu padziko lapansi,+Kuti aone ngati pali aliyense wozindikira, aliyense amene akufunafuna Yehova.+ Yesaya 43:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Koma iwe Yakobo, iwe Isiraeli, sunapemphe thandizo kwa ine+ chifukwa chakuti watopa nane.+ Aroma 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Palibe amene ali wozindikira ngakhale pang’ono, palibiretu amene akuyesetsa kupeza Mulungu.+
2 Koma kuchokera kumwamba, Yehova wayang’ana ana a anthu padziko lapansi,+Kuti aone ngati pali aliyense wozindikira, aliyense amene akufunafuna Yehova.+