Miyambo 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nsembe ya anthu oipa imam’nyansa Yehova,+ koma pemphero la anthu owongoka mtima limam’sangalatsa.+ Miyambo 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu amene amathawitsa khutu lake kuti asamve chilamulo,+ ngakhale pemphero lake limakhala lonyansa.+
9 Munthu amene amathawitsa khutu lake kuti asamve chilamulo,+ ngakhale pemphero lake limakhala lonyansa.+