Genesis 41:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ng’ombe 7 zowonda ndi zonyansazo, zimene zinatuluka pambuyo pa zoyamba zija, zikuimira zaka 7. Koma ngala 7 zimenezo, zopanda kanthu ndi zowauka ndi mphepo yakum’mawa,+ zidzakhala zaka 7 za njala.+ Amosi 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Ndinawononga mbewu zanu ndi mphepo yotentha komanso ndi matenda a chuku.+ Munachulukitsa minda yanu ya mpesa ndi ya mbewu zina ndipo mbozi zinawononga mitengo yanu ya mkuyu ndi ya maolivi,+ komabe inu simunabwerere kwa ine,’+ watero Yehova.
27 Ng’ombe 7 zowonda ndi zonyansazo, zimene zinatuluka pambuyo pa zoyamba zija, zikuimira zaka 7. Koma ngala 7 zimenezo, zopanda kanthu ndi zowauka ndi mphepo yakum’mawa,+ zidzakhala zaka 7 za njala.+
9 “‘Ndinawononga mbewu zanu ndi mphepo yotentha komanso ndi matenda a chuku.+ Munachulukitsa minda yanu ya mpesa ndi ya mbewu zina ndipo mbozi zinawononga mitengo yanu ya mkuyu ndi ya maolivi,+ komabe inu simunabwerere kwa ine,’+ watero Yehova.