Salimo 78:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Anapereka zokolola zawo kwa mphemvu,Ndipo ntchito yawo yolemetsa anaipereka kwa dzombe.+ Yeremiya 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chinthu chochititsa manyazi+ chadya ntchito yolemetsa ya manja a makolo athu kuyambira tili anyamata. Chadya nkhosa zawo, ng’ombe zawo, ana awo aamuna ndi ana awo aakazi.
24 Chinthu chochititsa manyazi+ chadya ntchito yolemetsa ya manja a makolo athu kuyambira tili anyamata. Chadya nkhosa zawo, ng’ombe zawo, ana awo aamuna ndi ana awo aakazi.