Deuteronomo 32:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Akanakhala anzeru,+ akanaganizira mozama zimenezi.+Akanalingalira kuti ziwathera bwanji.+ Hagai 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Ganizirani mofatsa zimene mukuchita.+