2 Mbiri 36:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova Mulungu wa makolo awo anapitiriza kuwatumizira machenjezo kudzera mwa amithenga ake.+ Anawatumiza mobwerezabwereza chifukwa ankamvera chisoni anthu akewo+ ndiponso malo ake okhala.+ Yeremiya 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 kuchokera tsiku limene makolo anu anatuluka m’dziko la Iguputo kufikira lero.+ Ndinapitiriza kukutumizirani atumiki anga onse aneneri, tsiku ndi tsiku ndinali kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza.+ Yeremiya 44:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndinali kukutumizirani atumiki anga onse aneneri, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza.+ Ndinali kuwatuma uthenga wakuti: “Chonde, musachite zinthu zonyansa zoterezi zimene ndimadana nazo.”+
15 Yehova Mulungu wa makolo awo anapitiriza kuwatumizira machenjezo kudzera mwa amithenga ake.+ Anawatumiza mobwerezabwereza chifukwa ankamvera chisoni anthu akewo+ ndiponso malo ake okhala.+
25 kuchokera tsiku limene makolo anu anatuluka m’dziko la Iguputo kufikira lero.+ Ndinapitiriza kukutumizirani atumiki anga onse aneneri, tsiku ndi tsiku ndinali kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza.+
4 Ine ndinali kukutumizirani atumiki anga onse aneneri, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza.+ Ndinali kuwatuma uthenga wakuti: “Chonde, musachite zinthu zonyansa zoterezi zimene ndimadana nazo.”+