Numeri 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chitsimechi n’chokumbidwa ndi akalonga. Chofukula anthu olemekezeka,Chofukula ndi ndodo ya mtsogoleri wa asilikali,+ chofukula ndi ndodo zawo.” Atachoka kuchipululucho anafika ku Matana. Aheberi 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwa chikhulupiriro, Yakobo ali pafupi kufa,+ anadalitsa ana aamuna a Yosefe mmodzimmodzi,+ ndipo analambira Mulungu atatsamira pamutu wa ndodo yake.+
18 Chitsimechi n’chokumbidwa ndi akalonga. Chofukula anthu olemekezeka,Chofukula ndi ndodo ya mtsogoleri wa asilikali,+ chofukula ndi ndodo zawo.” Atachoka kuchipululucho anafika ku Matana.
21 Mwa chikhulupiriro, Yakobo ali pafupi kufa,+ anadalitsa ana aamuna a Yosefe mmodzimmodzi,+ ndipo analambira Mulungu atatsamira pamutu wa ndodo yake.+