Salimo 103:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye sadzakhalira kutiimba mlandu nthawi zonse chifukwa cha zolakwa zathu,+Kapena kutisungira mkwiyo mpaka kalekale.+ Yesaya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 M’tsiku limenelo+ ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani inu Yehova pakuti ngakhale munandikwiyira, mkwiyo wanu unabwerera pang’onopang’ono+ ndipo munanditonthoza.+ Hagai 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi mbewu zilipobe m’dzenje losungiramo mbewu?+ Kodi mitengo ya mpesa, mitengo ya mkuyu, mitengo ya makangaza* ndi mitengo ya maolivi ikuberekabe zipatso? Kuyambira lero ndikupatsani madalitso.’”+
9 Iye sadzakhalira kutiimba mlandu nthawi zonse chifukwa cha zolakwa zathu,+Kapena kutisungira mkwiyo mpaka kalekale.+
12 M’tsiku limenelo+ ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani inu Yehova pakuti ngakhale munandikwiyira, mkwiyo wanu unabwerera pang’onopang’ono+ ndipo munanditonthoza.+
19 Kodi mbewu zilipobe m’dzenje losungiramo mbewu?+ Kodi mitengo ya mpesa, mitengo ya mkuyu, mitengo ya makangaza* ndi mitengo ya maolivi ikuberekabe zipatso? Kuyambira lero ndikupatsani madalitso.’”+