-
Zekariya 12:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Pa tsiku limenelo, ndidzachititsa mafumu a Yuda kukhala ngati mbaula zamoto pakati pa mitengo,+ komanso ngati miyuni yamoto pamilu ya tirigu wongodula kumene.+ Iwo adzatentha mitundu yonse ya anthu owazungulira, mbali ya kudzanja lamanja ndi kudzanja lamanzere.+ Anthu a mu Yerusalemu adzakhalabe mumzinda wawo wa Yerusalemu.+
-