Yesaya 66:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mudzaona zimenezi ndipo mtima wanu udzasangalala.+ Mafupa anu+ adzakhala ndi mphamvu ngati udzu wobiriwira.+ Dzanja la Yehova lidzadziwika kwa atumiki ake,+ koma iye adzakwiyira adani ake.”+ Zefaniya 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Fuula mosangalala iwe mwana wamkazi wa Ziyoni! Fuula mokondwera+ iwe Isiraeli! Sangalala ndi kukondwera ndi mtima wonse, iwe mwana wamkazi wa Yerusalemu!+
14 Mudzaona zimenezi ndipo mtima wanu udzasangalala.+ Mafupa anu+ adzakhala ndi mphamvu ngati udzu wobiriwira.+ Dzanja la Yehova lidzadziwika kwa atumiki ake,+ koma iye adzakwiyira adani ake.”+
14 Fuula mosangalala iwe mwana wamkazi wa Ziyoni! Fuula mokondwera+ iwe Isiraeli! Sangalala ndi kukondwera ndi mtima wonse, iwe mwana wamkazi wa Yerusalemu!+