Yesaya 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nsanje ya Efuraimu idzatha,+ ndipo ngakhale anthu odana ndi Yuda adzaphedwa. Efuraimu sadzachitira nsanje Yuda ndiponso Yuda sadzadana ndi Efuraimu.+ Ezekieli 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Koma iwe mwana wa munthu, tenga ndodo+ ndi kulembapo kuti, ‘Ndodo ya Yuda ndi anzake, ana a Isiraeli.’+ Utengenso ndodo ina ndi kulembapo kuti, ‘Ndodo ya Yosefe yoimira Efuraimu+ komanso anzawo onse a nyumba ya Isiraeli.’+
13 Nsanje ya Efuraimu idzatha,+ ndipo ngakhale anthu odana ndi Yuda adzaphedwa. Efuraimu sadzachitira nsanje Yuda ndiponso Yuda sadzadana ndi Efuraimu.+
16 “Koma iwe mwana wa munthu, tenga ndodo+ ndi kulembapo kuti, ‘Ndodo ya Yuda ndi anzake, ana a Isiraeli.’+ Utengenso ndodo ina ndi kulembapo kuti, ‘Ndodo ya Yosefe yoimira Efuraimu+ komanso anzawo onse a nyumba ya Isiraeli.’+