Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 2:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Munapitiriza kuchiyang’ana kufikira mwala unadulidwa kuphiri koma osati ndi manja a munthu.+ Mwalawo unamenya chifanizirocho kumapazi ake achitsulo chosakanizika ndi dongo ndipo unawapera.+

  • Danieli 2:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Zidzakhala choncho chifukwa munaona kuti mwala unadulidwa kuphiri koma osati ndi manja a munthu,+ ndipo unaphwanya chitsulo, mkuwa, dongo, siliva ndi golide.+ Inu mfumu, Mulungu Wamkulu+ wakudziwitsani zimene zidzachitike m’tsogolo.+ Maloto amenewa ndi odalirika ndipo kumasulira kwake ndi kokhulupirika.”+

  • Mateyu 21:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Komanso munthu wogwera pamwala umenewu adzaphwanyika. Ndipo aliyense amene mwalawo udzamugwere, udzamupereratu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena