Deuteronomo 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yehova adzakulanga ndi misala,+ khungu+ ndipo adzakuchititsa kudabwa kwambiri.+ Salimo 76:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Hatchi komanso wokwera galeta agona tulo tofa nato chifukwa cha kudzudzula kwanu, inu Mulungu wa Yakobo.+
6 Hatchi komanso wokwera galeta agona tulo tofa nato chifukwa cha kudzudzula kwanu, inu Mulungu wa Yakobo.+