Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 23:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 M’masiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa,+ ndipo Isiraeli adzakhala mwabata.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala Yehova Ndiye Chilungamo Chathu.”+

  • Yoweli 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Yehova adzabangula ngati mkango kuchokera m’Ziyoni ndipo adzalankhula ali ku Yerusalemu.+ Kumwamba ndi dziko lapansi zidzagwedezeka+ koma Yehova adzakhala chitetezo kwa anthu ake,+ ndipo adzakhala malo a chitetezo champhamvu kwa ana a Isiraeli.+

  • Zekariya 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ine ndidzamuzungulira ngati mpanda wake wamoto+ ndipo ndidzamudzaza ndi ulemerero wanga,”’ watero Yehova.”+

  • Zekariya 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova wa makamu adzatchinjiriza anthu ake. Adani awo adzawalasa ndi miyala yoponya ndi gulaye* koma iwo adzagonjetsa adaniwo.+ Iwo adzasangalala ndipo adzafuula ngati amwa vinyo.+ Adzadzazidwa ngati mbale zolowa ndiponso ngati mmene magazi amadzazira m’makona a guwa lansembe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena