Yesaya 65:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma kondwerani anthu inu,+ ndipo sangalalani kwamuyaya ndi zimene ndikulenga.+ Pakuti ndikulenga Yerusalemu kuti akhale chinthu chosangalatsa ndipo anthu ake akhale chinthu chokondweretsa.+ Aheberi 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma m’malomwake, inu mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda+ wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo miyandamiyanda,*+ Chivumbulutso 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinaonanso mzinda woyera,+ Yerusalemu Watsopano, ukutsika kuchokera kumwamba+ kwa Mulungu, utakonzedwa ngati mkwatibwi+ wokongoletsedwera mwamuna wake.+
18 Koma kondwerani anthu inu,+ ndipo sangalalani kwamuyaya ndi zimene ndikulenga.+ Pakuti ndikulenga Yerusalemu kuti akhale chinthu chosangalatsa ndipo anthu ake akhale chinthu chokondweretsa.+
22 Koma m’malomwake, inu mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda+ wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo miyandamiyanda,*+
2 Ndinaonanso mzinda woyera,+ Yerusalemu Watsopano, ukutsika kuchokera kumwamba+ kwa Mulungu, utakonzedwa ngati mkwatibwi+ wokongoletsedwera mwamuna wake.+