Nehemiya 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Eliyasibu+ mkulu wa ansembe ndi abale ake, ansembe, anayamba kumanga Chipata cha Nkhosa.+ Iwo anapatula mbali imeneyi+ ndi kuika zitseko zake. Anapatula mbali imeneyi mpaka ku Nsanja ya Meya+ ndi Nsanja ya Hananeli.+ Yeremiya 31:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Taonani! Masiku adzafika,” watero Yehova, “pamene anthu adzamangira+ Yehova mzinda kuyambira pa Nsanja ya Hananeli+ mpaka ku Chipata cha Pakona.+
3 Ndiyeno Eliyasibu+ mkulu wa ansembe ndi abale ake, ansembe, anayamba kumanga Chipata cha Nkhosa.+ Iwo anapatula mbali imeneyi+ ndi kuika zitseko zake. Anapatula mbali imeneyi mpaka ku Nsanja ya Meya+ ndi Nsanja ya Hananeli.+
38 “Taonani! Masiku adzafika,” watero Yehova, “pamene anthu adzamangira+ Yehova mzinda kuyambira pa Nsanja ya Hananeli+ mpaka ku Chipata cha Pakona.+