Ekisodo 12:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Lamulo lililonse ligwire ntchito mofanana kwa mbadwa ndi kwa mlendo wokhala pakati panu.”+ Salimo 82:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nyamukani inu Mulungu, weruzani dziko lapansi.+Pakuti inu nokha muyenera kutenga mitundu yonse kukhala yanu.+ Hagai 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Ndigwedeza mitundu yonse ya anthu, ndipo zinthu zamtengo wapatali zochokera ku mitundu yonse ya anthu zidzalowa m’nyumba imeneyi.+ Ine ndidzadzaza nyumbayi ndi ulemerero,’+ watero Yehova wa makamu.
8 Nyamukani inu Mulungu, weruzani dziko lapansi.+Pakuti inu nokha muyenera kutenga mitundu yonse kukhala yanu.+
7 “‘Ndigwedeza mitundu yonse ya anthu, ndipo zinthu zamtengo wapatali zochokera ku mitundu yonse ya anthu zidzalowa m’nyumba imeneyi.+ Ine ndidzadzaza nyumbayi ndi ulemerero,’+ watero Yehova wa makamu.